Movatterモバイル変換


[0]ホーム

URL:


Jump to content
Wikipedia
Fufuzani

United Kingdom

Kuchokera ku Wikipedia

United Kingdom wa Great Britain ndi Northern Ireland, wangotiUnited Kingdom kapenaUK, ndiboma lolamulira ku Northern Europe. Ndi ufumu wadziko lapansi womwe uli ndi mayiko anayi:England,Wales,Scotland ndiNorthern Ireland. Ndi membala waEuropean Union,United Nations, Commonwealth,NATO ndiG8. Ili ndi chuma chachisanu chachikulu padziko lonse lapansi.


Nkhaniyi ndistub. Mungathe kuthandiza Wikipedia ndikukulitsa izo.
Kuchotsahttps://ny.wikipedia.org/w/index.php?title=United_Kingdom&oldid=52752
Categories:

[8]ページ先頭

©2009-2025 Movatter.jp