Movatterモバイル変換


[0]ホーム

URL:


Jump to content
Wikipedia
Fufuzani

Tsamba Lalikulu

Kuchokera ku Wikipedia

Mwalandilidwa paWikipedia,
encyclopedia yaulere imene aliyense angathandizile kukuza!
Pakali pano tili ndi nkhani zokwana1,099 muchiChewa, chinenero chomwe chimayankhulidwa kuMalawi ndiZambia.

Za Wikipedia

  • Wikipedia ya Chichewa ndi buku laulere. Ndi wiki, mtundu wa webusaiti yomwe anthu ambiri amawalemba. Izi zikutanthawuza kuti aliyense angathe kusintha tsamba lirilonse podalira pa "kusintha tsamba lino". Mungathe kuchita izi pa tsamba lirilonse losatetezedwa. Mukhoza kuona ngati tsambalo liri kutetezedwa chifukwa lidzati "View source" mmalo mwa "Sintha".

Mukamalemba nkhani apa

  • Lembani masamba abwino. Masamba abwino kwambiri a encyclopedia ali ndi zothandiza, zolembedwa bwino.
  • Osagwilitsa ntchito makina ngati google translator! Nkhani yolembedwa pogwilitsa ntchitotranslator wina aliyense siikhala yomveka bwino (Don't use machine translations!). Nkhani zotelo zizafufutidwa pano mopanda kudziwitsa olembayo komanso kupitiliza kutelo n'kuphwanya malamulo a Wikipediya.
  • Gwiritsani ntchito masambawa kuti muphunzire ndi kuphunzitsa. Masambawa angathandize anthu kuphunzira Chichewa. Mutha kuigwiritsanso ntchitopangani Wikipedia yatsopano kuthandiza anthu ena.
  • Khalani wolimba! Nkhani yanu siyenela kukhala yangwiro, chifukwa olemba ena adzakonza ndikupanga bwino. Ndipo chofunika kwambiri, musaope kuyamba ndi kupanga nkhani bwino.

Mu nkhani

Chithunzi cha tsikulo

Chithunzi chili osapezeka lero.

Wikipedia Muzinenero Zina

Wikipedia iyi yalembedwa mu Chichewa. Kuyambira mu 2001, pakali pano muli nkhani1,099. Ma Wikipedias ambiri amapezeka; ma Wikipediya ena amu Afrika ali pansipa.

Afrikaans |Luganda |Gĩkũyũ |Hausa |Igbo |KiKongo |Lingala |Kirundi |Ikinyarwanda |chiShona |Sesotho |Sesotho sa leboa |Kiswahili |SiSwati |Xitsonga |Setswana |chiTumbuka |Tshivenda |isiXhosa |Yorùbá |

Ntchito zina za Wikimedia

Wikipedia imayang'aniridwa ndiWikimedia Foundation, bungwe lopanda phindu lomwe limakhalanso ndimapulojekiti:
Commons
Malo omwe aliyense angapeze ndikugawana zithunzi, makanema, ndi mawu aulere.
Wikifunctions
Malo omwe mungapeze ndikugwiritsa ntchito zida zothandiza ndi njira zazifupi pantchito zosiyanasiyana.
Wikidata
Malo omwe chidziwitso chimakonzedwa ndikusungidwa m'njira yoti aliyense azitha kuzipeza ndikuzigwiritsa ntchito momasuka.
Wikispecies
Mndandanda wa nyama zosiyanasiyana, zomera, ndi zamoyo zina.
Wikipedia
Buku lalikulu lapaintaneti lodzaza ndi zambiri zolembedwa mchingerezi zomwe aliyense angaziwerenge ndikuwongolera.
Wikiquote
Malo omwe mungapezeko mawu otchuka komanso osangalatsa ochokera kwa anthu.
Wikinews
Nkhani zomwe aliyense angathe kuziwerenga, kugawana, ndi kuthandiza kulemba.
Wiktionary
Dictionary and thesaurus
Wikiversity
Zida zaulere monga mabuku, makanema, ndi maupangiri omwe amakuthandizani kuphunzira zinthu zatsopano.
Wikibooks
Malo omwe mungapeze mabuku ndi malangizo okuthandizani kuphunzira, ndipo ndi omasuka kugwiritsa ntchito.
Wikisource
Laibulale komwe mungapeze mabuku, zithunzi, ndi zinthu zina zaulere kuti aliyense azigwiritsa ntchito.
MediaWiki
Malo omwe anthu amagwira ntchito popanga ndi kukonza mapulogalamu omwe amayendetsa Wikipedia ndi mawebusayiti ena a Wiki.
Meta-Wiki
Malo oti anthu ogwira ntchito pa Wikipedia ndi ma projekiti ena akonzekere, kukonza, ndi kugwirira ntchito limodzi.
Wikivoyage
Upangiri waulere womwe umakuthandizani kuti muphunzire za malo omwe mungayendere, zinthu zoti muchite, komanso momwe mungayendere.

Onaninso masamba aWikimedia Foundation Governance wiki, nawonso.

Purge server cache

Kuchotsahttps://ny.wikipedia.org/w/index.php?title=Tsamba_Lalikulu&oldid=55791

[8]ページ先頭

©2009-2025 Movatter.jp